Genesis 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+ Deuteronomo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adzachita zimenezi popeza udzamvera mawu a Yehova Mulungu wako ndi kusunga malamulo ake ndi mfundo zake zolembedwa m’buku ili la chilamulo,+ chifukwa udzabwerera kwa Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse.+
5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+
10 Adzachita zimenezi popeza udzamvera mawu a Yehova Mulungu wako ndi kusunga malamulo ake ndi mfundo zake zolembedwa m’buku ili la chilamulo,+ chifukwa udzabwerera kwa Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse.+