Salimo 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Monga mmene mbawala yaikazi imalakalakira mitsinje ya madzi,Moyo wanganso ukulakalaka inu Mulungu wanga.+ Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuMādziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+
42 Monga mmene mbawala yaikazi imalakalakira mitsinje ya madzi,Moyo wanganso ukulakalaka inu Mulungu wanga.+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuMādziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+