Yobu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sindisiya malamulo otuluka pakamwa pake.+Ndasunga mosamala mawu a pakamwa pake+ kuposa zimene akufuna kuti ndichite. Salimo 119:174 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 174 Ndikulakalaka chipulumutso chanu, inu Yehova,+Ndipo ndimakonda kwambiri chilamulo chanu.+ Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga+ ndimasangalala kwambiri+ ndi chilamulo cha Mulungu,
12 Sindisiya malamulo otuluka pakamwa pake.+Ndasunga mosamala mawu a pakamwa pake+ kuposa zimene akufuna kuti ndichite.