Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+ Salimo 119:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzakonda malamulo anu.+Ndipo sindidzaiwala mawu anu.+
2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+