Deuteronomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+ Yohane 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Anthu amene munawatenga m’dziko ndi kundipatsa ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine, ndipo iwo asunga mawu anu. Yakobo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti ngati munthu ali wongomva mawu, koma wosachita,+ ali ngati munthu wodziyang’anira nkhope yake pagalasi.
13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+
6 “Anthu amene munawatenga m’dziko ndi kundipatsa ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine, ndipo iwo asunga mawu anu.
23 Pakuti ngati munthu ali wongomva mawu, koma wosachita,+ ali ngati munthu wodziyang’anira nkhope yake pagalasi.