Salimo 94:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Malingaliro osautsa atandichulukira mumtima mwanga,+Mawu anu otonthoza anayamba kusangalatsa moyo wanga.+ Aroma 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+
19 Malingaliro osautsa atandichulukira mumtima mwanga,+Mawu anu otonthoza anayamba kusangalatsa moyo wanga.+
4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+