Salimo 71:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kulitsani ulemu wanga,+Mundizungulire ndi chitetezo chanu ndi kundilimbikitsa.+ Salimo 86:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ikani chizindikiro cha ubwino wanu pa ine,Kuti anthu odana nane aone zimenezi ndi kuchita manyazi,+Pakuti inu Yehova mwandithandiza ndi kundilimbikitsa.+
17 Ikani chizindikiro cha ubwino wanu pa ine,Kuti anthu odana nane aone zimenezi ndi kuchita manyazi,+Pakuti inu Yehova mwandithandiza ndi kundilimbikitsa.+