Salimo 99:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu anapitiriza kulankhula nawo mumtambo woima njo ngati chipilala.+Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malangizo amene anawapatsa.+ Salimo 119:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Odala ndi anthu amene amasunga zikumbutso zake,+Amene amayesetsa kumufunafuna ndi mtima wonse.+
7 Mulungu anapitiriza kulankhula nawo mumtambo woima njo ngati chipilala.+Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malangizo amene anawapatsa.+