1 Mafumu 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Eliya anayandikira anthu onsewo n’kunena kuti: “Kodi mukayikakayika* mpaka liti?+ Ngati Yehova ali Mulungu woona m’tsateni,+ koma ngati Baala ndiye Mulungu woona tsatirani ameneyo.” Koma anthuwo sanamuyankhe chilichonse. 2 Mafumu 17:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mitundu imeneyi inali kuopa Yehova,+ koma inali kutumikira zifaniziro zawo zogoba. Mpaka lero, ana awo ndi zidzukulu zawo akuchitabe mmene makolo awo ankachitira. Chivumbulutso 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, chifukwa choti ndiwe wofunda, osati wotentha+ kapena wozizira,+ ndikulavula m’kamwa mwanga.
21 Kenako Eliya anayandikira anthu onsewo n’kunena kuti: “Kodi mukayikakayika* mpaka liti?+ Ngati Yehova ali Mulungu woona m’tsateni,+ koma ngati Baala ndiye Mulungu woona tsatirani ameneyo.” Koma anthuwo sanamuyankhe chilichonse.
41 Mitundu imeneyi inali kuopa Yehova,+ koma inali kutumikira zifaniziro zawo zogoba. Mpaka lero, ana awo ndi zidzukulu zawo akuchitabe mmene makolo awo ankachitira.
16 Choncho, chifukwa choti ndiwe wofunda, osati wotentha+ kapena wozizira,+ ndikulavula m’kamwa mwanga.