-
Ezara 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 nthawi yomweyo anapita kwa Zerubabele+ ndi kwa atsogoleri+ a nyumba za makolo n’kukawauza kuti: “Bwanji timangire nanu limodzi,+ popeza ifeyo mofanana ndi inuyo, timapembedza Mulungu wanu+ ndipo timapereka nsembe kwa iye, kuyambira m’masiku a Esari-hadoni+ mfumu ya Asuri, yemwe anatibweretsa kuno.”+
-