Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ankaopa Yehova+ koma ankalambira milungu yawo,+ mogwirizana ndi chipembedzo cha mitundu imene anawatengako.+

  • 2 Mafumu 17:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Mpaka lero akutsatirabe zipembedzo zawo zakale.+ Palibe amene ankaopa Yehova+ ndipo palibe amene ankatsatira malamulo ake, zigamulo zake,+ ndi chilamulo+ chimene Yehova analamula ana a Yakobo.+ Yakoboyo Mulungu anamusintha dzina n’kumutcha Isiraeli,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena