Ezara 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400 ndipo Sezibazara+ anabweretsa zonsezi ku Yerusalemu. Anatenganso anthu amene anagwidwa ukapolo+ kuchoka nawo ku Babulo n’kupita nawo ku Yerusalemu. Ezara 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amenewa anabwera pamodzi ndi Zerubabele,+ Yesuwa,*+ Nehemiya, Seraya,+ Reelaya, Moredekai, Bilisani, Misipara, Bigivai, Rehumu, ndi Bana. Chiwerengero cha amuna a Isiraeli chinali ichi:
11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400 ndipo Sezibazara+ anabweretsa zonsezi ku Yerusalemu. Anatenganso anthu amene anagwidwa ukapolo+ kuchoka nawo ku Babulo n’kupita nawo ku Yerusalemu.
2 Amenewa anabwera pamodzi ndi Zerubabele,+ Yesuwa,*+ Nehemiya, Seraya,+ Reelaya, Moredekai, Bilisani, Misipara, Bigivai, Rehumu, ndi Bana. Chiwerengero cha amuna a Isiraeli chinali ichi: