Salimo 93:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zikumbutso zanu ndi zodalirika zedi.+Chiyero ndi choyenera nyumba yanu+ mpaka muyaya, inu Yehova.+ Salimo 119:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Odala ndi anthu amene amasunga zikumbutso zake,+Amene amayesetsa kumufunafuna ndi mtima wonse.+