Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+ Salimo 71:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+ Salimo 145:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo adzalankhula mosefukira za kuchuluka kwa ubwino wanu,+Ndipo adzafuula mokondwera chifukwa cha chilungamo chanu.+ Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+
5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+
17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+
7 Iwo adzalankhula mosefukira za kuchuluka kwa ubwino wanu,+Ndipo adzafuula mokondwera chifukwa cha chilungamo chanu.+
14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+