Salimo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+ Salimo 119:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndasunga mosamala mawu anu mumtima mwanga,+Kuti ndisakuchimwireni.+
9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+