Nehemiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, imvani+ mawu onyoza amene akutinenera.+ Bwezerani chitonzo chawocho+ pamutu pawo ndipo apititseni m’dziko laukapolo monga zofunkha. Salimo 44:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+ Salimo 89:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Inu Yehova, kumbukirani mmene adani anu alankhulira motonza,+Mmene atonzera paliponse pamene mapazi a wodzozedwa wanu aponda.+
4 Ndiyeno Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, imvani+ mawu onyoza amene akutinenera.+ Bwezerani chitonzo chawocho+ pamutu pawo ndipo apititseni m’dziko laukapolo monga zofunkha.
13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+
51 Inu Yehova, kumbukirani mmene adani anu alankhulira motonza,+Mmene atonzera paliponse pamene mapazi a wodzozedwa wanu aponda.+