Salimo 56:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndikomereni mtima inu Mulungu wanga, chifukwa munthu wopanda pake akufuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+Akulimbana nane tsiku lonse ndi kundipondereza.+ Salimo 76:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mkwiyo wa munthu udzakutamandani,+Mkwiyo wake wotsala mudzaumangirira m’chiuno mwanu. Miyambo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tiye tikawameze amoyo+ ngati mmene amachitira Manda,*+ tikawameze athunthu ngati amene akupita kudzenje.+
56 Ndikomereni mtima inu Mulungu wanga, chifukwa munthu wopanda pake akufuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+Akulimbana nane tsiku lonse ndi kundipondereza.+
12 Tiye tikawameze amoyo+ ngati mmene amachitira Manda,*+ tikawameze athunthu ngati amene akupita kudzenje.+