Salimo 118:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munandikankha kwambiri kuti ndigwe,+Koma Yehova anandithandiza.+ Salimo 125:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndodo yachifumu ya oipa sidzapitiriza kukhala+ padziko limene olungama analandira monga cholowa chawo,Kuti olungamawo asatambasule dzanja lawo ndi kuchita choipa.+ Yohane 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndanena zimenezi kwa inu kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ M’dzikomu mukumana ndi masautso, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+
3 Ndodo yachifumu ya oipa sidzapitiriza kukhala+ padziko limene olungama analandira monga cholowa chawo,Kuti olungamawo asatambasule dzanja lawo ndi kuchita choipa.+
33 Ndanena zimenezi kwa inu kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ M’dzikomu mukumana ndi masautso, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+