Ekisodo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+ Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+ Aroma 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Odala ndi amene akhululukidwa zochita zawo zosamvera malamulo+ ndipo machimo awo aphimbidwa.+
7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+
11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+