Deuteronomo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Asidoni anali kutcha phiri la Herimoni kuti Sirioni,+ pamene Aamori anali kulitcha kuti Seniri.)+ Deuteronomo 4:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ m’mphepete mwa chigwa* cha Arinoni mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+ 1 Mbiri 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana a hafu ya fuko la Manase+ anakhala m’dera loyambira ku Basana+ mpaka ku Baala-herimoni,+ ku Seniri,+ ndi kuphiri la Herimoni,+ ndipo iwo anachulukana kwambiri.
48 Dera limeneli linayambira ku Aroweli+ m’mphepete mwa chigwa* cha Arinoni mpaka kuphiri la Sione, limene ndi phiri la Herimoni,+
23 Ana a hafu ya fuko la Manase+ anakhala m’dera loyambira ku Basana+ mpaka ku Baala-herimoni,+ ku Seniri,+ ndi kuphiri la Herimoni,+ ndipo iwo anachulukana kwambiri.