Levitiko 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Dziwani kuti ndidzakudalitsani m’chaka cha 6, ndipo dzikolo lidzakupatsani chakudya cha zaka zitatu.+ Deuteronomo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzaika madalitso pankhokwe+ ndi pa zochita zako zonse+ ndipo adzakudalitsa m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.
21 Dziwani kuti ndidzakudalitsani m’chaka cha 6, ndipo dzikolo lidzakupatsani chakudya cha zaka zitatu.+
8 Yehova adzaika madalitso pankhokwe+ ndi pa zochita zako zonse+ ndipo adzakudalitsa m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.