Salimo 92:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+Ndi kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+ Salimo 147:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 147 Tamandani Ya, anthu inu,+Pakuti kuimbira Mulungu wathu nyimbo zomutamanda n’kwabwino,+Ndipo n’kosangalatsa. Kumutamanda n’koyenera.+
92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+Ndi kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+ Salimo 147:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 147 Tamandani Ya, anthu inu,+Pakuti kuimbira Mulungu wathu nyimbo zomutamanda n’kwabwino,+Ndipo n’kosangalatsa. Kumutamanda n’koyenera.+
147 Tamandani Ya, anthu inu,+Pakuti kuimbira Mulungu wathu nyimbo zomutamanda n’kwabwino,+Ndipo n’kosangalatsa. Kumutamanda n’koyenera.+