Salimo 92:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+Ndi kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+ Salimo 135:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamandani Ya, pakuti Yehova ndi wabwino.+Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti kuchita zimenezi n’kosangalatsa.+
92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+Ndi kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+ Salimo 135:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamandani Ya, pakuti Yehova ndi wabwino.+Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti kuchita zimenezi n’kosangalatsa.+
3 Tamandani Ya, pakuti Yehova ndi wabwino.+Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti kuchita zimenezi n’kosangalatsa.+