Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Yobu 38:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndani anaika nzeru+ m’mitambo,Kapena zinthu zochitika kuthambo, ndani anazipatsa kuzindikira?+ Miyambo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anayala maziko a dziko lapansi mwanzeru.+ Anakhazikitsa kumwamba mozindikira.+ Yeremiya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru zake+ anakhazikitsa dziko limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+ Yeremiya 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru+ zake anakhazikitsa dziko+ limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+
12 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru zake+ anakhazikitsa dziko limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+
15 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru+ zake anakhazikitsa dziko+ limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+