Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,

      Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+

      Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+

      Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+

  • Yona 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pamene ndinalefuka kwambiri,+ ndinakumbukira Yehova.+

      Ndipo pemphero langa linafika kwa inu, m’kachisi wanu woyera.+

  • Maliko 15:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndipo cha m’ma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+

  • Aheberi 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena