Salimo 77:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzakumbukira zochita za Ya,+Ndithu ndidzakumbukira ntchito yanu yodabwitsa yakale.+ Salimo 143:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakumbukira masiku akale.+Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+ 2 Akorinto 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngakhalenso m’mitima mwathu, tinali kumva ngati talandira chiweruzo cha imfa. Zinatero kuti tisakhale ndi chikhulupiriro mwa ife tokha,+ koma mwa Mulungu amene amaukitsa akufa.+
5 Ndakumbukira masiku akale.+Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+
9 Ngakhalenso m’mitima mwathu, tinali kumva ngati talandira chiweruzo cha imfa. Zinatero kuti tisakhale ndi chikhulupiriro mwa ife tokha,+ koma mwa Mulungu amene amaukitsa akufa.+