Salimo 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Moyo wathu wakhala ukuyembekeza Yehova.+Iye ndi mthandizi wathu ndi chishango chathu.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+ 2 Akorinto 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ndimasangalala ndi kufooka, zitonzo, zosowa zanga, mazunzo ndi zovuta zina, chifukwa cha Khristu. Pakuti pamene ndili wofooka, m’pamene ndimakhala wamphamvu.+
10 Chotero ndimasangalala ndi kufooka, zitonzo, zosowa zanga, mazunzo ndi zovuta zina, chifukwa cha Khristu. Pakuti pamene ndili wofooka, m’pamene ndimakhala wamphamvu.+