1 Mafumu 18:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+
45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+