Salimo 63:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwabwino kuposa moyo,+Milomo yanga idzakuyamikirani.+ Salimo 117:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 117 Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+Mulemekezeni, inu mafuko onse.+