Levitiko 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu+ akachimwa mosadziwa+ mwa kuchita zinthu zimene Yehova analamula kuti musachite, iye akachita chimodzi mwa zimenezo muzichita izi: Salimo 90:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu+ akachimwa mosadziwa+ mwa kuchita zinthu zimene Yehova analamula kuti musachite, iye akachita chimodzi mwa zimenezo muzichita izi:
8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+