Genesis 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano zimenezi zitapita, Mulungu woona anamuyesa Abulahamu+ pomuuza kuti: “Abulahamu!” Iye anayankha kuti: “Ine mbuyanga!”+ Salimo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+
22 Tsopano zimenezi zitapita, Mulungu woona anamuyesa Abulahamu+ pomuuza kuti: “Abulahamu!” Iye anayankha kuti: “Ine mbuyanga!”+
9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+