Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Salimo 95:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tiyeni tionekere pamaso pake ndi chiyamiko.+Tiyeni tiimbe nyimbo zomutamanda ndi kumufuulira mosangalala chifukwa wapambana.+
23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
2 Tiyeni tionekere pamaso pake ndi chiyamiko.+Tiyeni tiimbe nyimbo zomutamanda ndi kumufuulira mosangalala chifukwa wapambana.+