Salimo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+ Salimo 119:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndayesetsa ndi mtima wanga wonse kuti mundiyanje.*+Ndikomereni mtima monga mwa mawu anu.+
2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+