Salimo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+ Salimo 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Mulungu ndiye mthandizi wanga.+Yehova ali pakati pa anthu amene akuchirikiza moyo wanga.
7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+