Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 tsiku limene adzagawa zinthu zake monga cholowa kwa ana ake aamuna, sadzaloledwa kutenga mwana wamwamuna wa mkazi wokondedwa uja ngati mwana wake woyamba kubadwa m’malo mwa mwana wamwamuna wa mkazi wosakondedwayo, amene ndiyedi woyamba kubadwa.+

  • 2 Akorinto 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kanotu ndi kachitatu+ kukhala wokonzeka kubwera kwa inu, koma sindidzakhala katundu wolemetsa. Pakuti sindikufuna zinthu zanu,+ koma inuyo. Paja ana+ sayenera kusunga chuma kuti chidzathandize makolo awo m’tsogolo, koma makolo ndi amene ayenera kusungira ana awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena