1 Akorinto 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sikuti ndikulemba zinthu zimenezi kuti ndikuchititseni manyazi, koma kuti ndikulangizeni monga ana anga okondedwa.+ Agalatiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndiye kuti n’zabwino kwa inu ana anga.+ Ine ndayambanso kumva zopweteka zimene ndinamva pokuberekani, mpaka Khristu adzakhazikike mwa inu.+
14 Sikuti ndikulemba zinthu zimenezi kuti ndikuchititseni manyazi, koma kuti ndikulangizeni monga ana anga okondedwa.+
19 ndiye kuti n’zabwino kwa inu ana anga.+ Ine ndayambanso kumva zopweteka zimene ndinamva pokuberekani, mpaka Khristu adzakhazikike mwa inu.+