Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+

  • Mlaliki 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chimene chimamvetsa chisoni pa zinthu zonse zimene zimachitika padziko lapansi pano n’chakuti, popeza mapeto a anthu onse ndi amodzi,+ mtima wa ana a anthu ndi wodzazanso ndi zoipa.+ Mumtima mwawo mumakhala misala+ pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo pamapeto pake, iwo amapita kwa akufa.+

  • Aefeso 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena