Miyambo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kulungama kwa munthu wopanda cholakwa n’kumene kudzawongole njira yake,+ koma woipa adzagwera m’zoipa zakezo.+ 1 Atesalonika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Mulungu wathu ndi Atate mwiniyo, ndi Ambuye wathu Yesu,+ atitsogolere pa ulendo wathu wobwera kwa inu kuti zonse ziyende bwino.
5 Kulungama kwa munthu wopanda cholakwa n’kumene kudzawongole njira yake,+ koma woipa adzagwera m’zoipa zakezo.+
11 Tsopano Mulungu wathu ndi Atate mwiniyo, ndi Ambuye wathu Yesu,+ atitsogolere pa ulendo wathu wobwera kwa inu kuti zonse ziyende bwino.