Yobu 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inutu mukhoza kuchita maere kuti mutenge mwana wamasiye,+Ndipo mnzanu mukhoza kumugulitsa.+ Salimo 94:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amapha mkazi wamasiye ndi mlendo wokhala m’dziko lawo,+Ndipo amaphanso ana amasiye.*+ Yeremiya 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ngati simudzapondereza mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye,+ komanso ngati simudzakhetsa magazi a munthu wopanda mlandu m’dziko lino,+ ndiponso ngati simudzatsatira milungu ina, zimene zingakubweretsereni tsoka,+
6 ngati simudzapondereza mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye,+ komanso ngati simudzakhetsa magazi a munthu wopanda mlandu m’dziko lino,+ ndiponso ngati simudzatsatira milungu ina, zimene zingakubweretsereni tsoka,+