Yesaya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka m’mawa kuti akafunefune chakumwa choledzeretsa.+ Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.+
11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka m’mawa kuti akafunefune chakumwa choledzeretsa.+ Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.+