Yesaya 65:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Koma anthu inu mwamusiya Yehova.+ Mwaiwala phiri langa loyera.+ Inu mumayalira tebulo mulungu wa Mwayi.+ Mumadzaza chikho ndi vinyo wosakaniza n’kupereka kwa mulungu wa Zokonzedweratu.+
11 “Koma anthu inu mwamusiya Yehova.+ Mwaiwala phiri langa loyera.+ Inu mumayalira tebulo mulungu wa Mwayi.+ Mumadzaza chikho ndi vinyo wosakaniza n’kupereka kwa mulungu wa Zokonzedweratu.+