2 Mbiri 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kuwonjezera apo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya+ za m’nyumba ya Mulungu woona+ n’kuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko+ za nyumba ya Yehova. Kenako anakadzimangira maguwa ansembe m’makona onse a mu Yerusalemu.+ 2 Mbiri 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 chifukwa chakuti andisiya+ n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho nditsanulira mkwiyo wanga+ pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+
24 Kuwonjezera apo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya+ za m’nyumba ya Mulungu woona+ n’kuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko+ za nyumba ya Yehova. Kenako anakadzimangira maguwa ansembe m’makona onse a mu Yerusalemu.+
25 chifukwa chakuti andisiya+ n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho nditsanulira mkwiyo wanga+ pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+