1 Mafumu 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zitseko ziwirizo zinali za matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza.+ Zitseko ziwiri za khomo limodzi zinkayenda pamiyendo yake, ndipo zitseko ziwiri za khomo linalo zinkayendanso pamiyendo yake.+ 2 Mbiri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatseka zitseko+ za khonde, anazimitsa nyale,+ ndiponso anasiya kupsereza zofukiza+ ndi kupereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli m’malo oyera.+
34 Zitseko ziwirizo zinali za matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza.+ Zitseko ziwiri za khomo limodzi zinkayenda pamiyendo yake, ndipo zitseko ziwiri za khomo linalo zinkayendanso pamiyendo yake.+
7 Anatseka zitseko+ za khonde, anazimitsa nyale,+ ndiponso anasiya kupsereza zofukiza+ ndi kupereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli m’malo oyera.+