2 Mbiri 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo+ m’mabwalo+ awiri a nyumba ya Yehova.+ Yeremiya 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Kodi milungu yako imene wadzipangira ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka.+ Pakuti iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+
5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo+ m’mabwalo+ awiri a nyumba ya Yehova.+
28 “Kodi milungu yako imene wadzipangira ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka.+ Pakuti iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+