Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Usadane ndi m’bale wako mumtima mwako.+ Mnzako um’dzudzule ndithu+ kuti usasenze naye tchimo. Mateyu 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+
15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+