Miyambo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse,+ ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.+ Miyambo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+ Mateyu 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kenako anatambasula dzanja lake ndi kuloza ophunzira ake, n’kunena kuti: “Ona! Mayi anga ndi abale anga!+
17 Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse,+ ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.+
24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+
49 Kenako anatambasula dzanja lake ndi kuloza ophunzira ake, n’kunena kuti: “Ona! Mayi anga ndi abale anga!+