Miyambo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Siliva amamuyengera m’mbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera m’ng’anjo,+ koma Yehova ndiye amene amayesa mitima.+
3 Siliva amamuyengera m’mbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera m’ng’anjo,+ koma Yehova ndiye amene amayesa mitima.+