Yobu 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngakhale akonze zovalazo, wolungama ndi amene adzazivale.+Ndipo silivayo, wosalakwa ndi amene adzam’tenge. Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+ Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wokomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+ ndipo adzam’bwezera zimene anachitazo.+
17 Ngakhale akonze zovalazo, wolungama ndi amene adzazivale.+Ndipo silivayo, wosalakwa ndi amene adzam’tenge.
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+