Salimo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Wodala+ ndi munthu amene sayenda motsatira malangizo a anthu oipa,+Saima m’njira ya anthu ochimwa,+Ndipo sakhala pansi pamodzi ndi anthu onyoza.+ Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+
1 Wodala+ ndi munthu amene sayenda motsatira malangizo a anthu oipa,+Saima m’njira ya anthu ochimwa,+Ndipo sakhala pansi pamodzi ndi anthu onyoza.+