Salimo 119:115 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 115 Ndichokereni anthu ochita zoipa inu,+Kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga.+ Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+